Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu adzapatsa mvula ya mbeu yako, ukaibzale m'nthaka; ndi mkate ndiwo phindu la nthaka, ndipo tirigu wace adzaca bwino ndi kucuruka; tsiku limenelo ng'ombe zako zidzadya m'madambo akuru.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:23 nkhani