Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 3:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. mbera, ndi makoza, ndi nsaru za pankhope;

20. ndi zisada, ndi maunyolo a kumwendo, ndi mipango, ndi nsupa zonunkhira, ndi mphinjiri;

21. mphete, ndi zipini;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 3