Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 3:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu anga awabvuta ndi ana, awalamulira ndi akazi. Anthu anga inu, iwo amene akutsogolerani, ndiwo akucimwitsani, naononga njira zanu zoyendamo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 3

Onani Yesaya 3:12 nkhani