Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo onani, Ambuye, Yehova wa makamu, wacotsa ku Yerusalemu ndi ku Yuda mcirikizo wocirikiza cakudya conse ndi madzi onse, zimene zinali mcirikizo;

2. munthu wamphamvu, ndi munthu wankhondo; woweruza, ndi mneneri, ndi waula, ndi nkhalamba;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 3