Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 29:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene iye aona ana ace, nchito ya manja anga, pakati pa iye, iwo adzayeretsa dzina langa; inde, iwo adzayeretsa Woyera wa Yakobo, nadzaopa Mulungu wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 29

Onani Yesaya 29:23 nkhani