Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 29:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ozolitsa inu! Kodi woumba adzayesedwa ngati dothi; kodi cinthu copangidwa cinganene za iye amene anacipanga, Iye sanandipanga ine konse; kapena kodi cinthu coumbidwa cinganene za iye amene anaciumba, Iye alibe nzeru?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 29

Onani Yesaya 29:16 nkhani