Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 29:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova watsanulira pa inu mzimu wa tulo togonetsa, natseka maso anu, ndiwo aneneri; naphimba mitu yanu, ndiwo alauli.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 29

Onani Yesaya 29:10 nkhani