Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 28:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti sapuntha mawere ndi copunthira cakuthwa, ngakhale kuzunguniza njinga ya gareta pacitowe; koma amakulunga mawere ndi munsi, naomba citowe ndi cibonga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 28

Onani Yesaya 28:27 nkhani