Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 27:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mibadwo ikudzayo Yakobo adzamera mizu; Israyeli adzaphuka ndi kucita mphundu; ndipo iwo adzadzaza ndi zipatso pa dziko lonse lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 27

Onani Yesaya 27:6 nkhani