Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 24:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kucokera ku malekezero a dziko ife tamva nyimbo zolemekeza wolungama. Koma ine ndinati, Ndaonda ine, ndaonda ine, tsoka kwa ine! amalonda onyenga amangonyenga; inde ogulitsa onyenga apambana kunyenga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 24

Onani Yesaya 24:16 nkhani