Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 23:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, dziko la Akasidi; anthu awa sakhalanso; Asuri analiika ilo likhale la iwo okhala m'cipululu; iwo amanga nsanja zao, nagumula nyumba za mafumu ace; nalipasula.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 23

Onani Yesaya 23:13 nkhani