Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 22:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye ndithu adzakuzunguza, ndi kukuponyaponya ngati mpira m'dzido lalikuru; kumeneko iwe udzafa, ndipo kumeneko kudzakhala magareta a ulemerero wako, iwe wocititsa manyazi banja la mbuye wako.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 22

Onani Yesaya 22:18 nkhani