Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 21:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo taonani, kuno kulinkudza khamu la amuna, apaakavalo awiri awiri. Ndipo iye anayankha nati, Babulo wagwa, wagwa; ndi mafano onse osema a milungu yace asweka, nagwa pansi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 21

Onani Yesaya 21:9 nkhani