Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 20:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wokhala m'mphepete mwa nyanja muno adzati tsiku limenelo, Taonani, kuyembekeza kwathu kuli kotero, kumene ife tinathawira atithangate kupulumutsidwa kwa mfumu ya Asuri, ndipo ife tidzapulumuka bwanji?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 20

Onani Yesaya 20:6 nkhani