Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 20:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

momwemo mfumu ya Asuri idzatsogolera kwina am'nsinga a Aigupto, ndi opitikitsidwa a Etiopia, ana ndi okalamba, amarisece ndi opanda nsapato, ndi matako osabvala, kuti acititse manyazi Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 20

Onani Yesaya 20:4 nkhani