Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 2:15-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. ndi pa nsanja zazitari zonse, ndi pa macemba onse;

16. ndi pa ngalawa zonse za Tarisi, ndi pa zithunzithunzi zonse zokondweretsa.

17. Ndipo kudzikweza kwa munthu kudzaweramitsidwa pansi, kudzikuza kwa munthu kudzatsitsidwa; ndipo Yehova yekha adzakwezedwa tsiku limenelo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 2