Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 19:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzadziwika kwa Aigupto, ndipo Aaigupto adzadziwa Yehova tsiku limenelo; inde iwo adzapembedzera ndi nsembe ndi zopereka, nadzawindira Yehova ndi kucitadi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 19

Onani Yesaya 19:21 nkhani