Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mudzasiyidwa m'menemo khunkha, monga ngati kugwedeza kwace kwa mtengo waazitona, zipatso ziwiri pena zitatu m'nsonga ya nthambi yosomphoka, zinai pena zisanu m'nthambi za kunthemba, za mtengo wobalitsa, ati Yehova, Mulungu wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 17

Onani Yesaya 17:6 nkhani