Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 17:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mitundu ya anthu idzathamanga ngati kuthamanga kwa madzi ambirimbiri; koma Iye adzawadzudzula, ndipo iwo adzathawira patari, nadzapitikitsidwa monga mankhusu a pamapiri patsogolo pa mphepo, ndi monga pfumbi lokwetera patsogolo pa mkunthu wa mphepo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 17

Onani Yesaya 17:13 nkhani