Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 14:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunsi kwa manda kugwedezeka, cifukwa ca iwe, kukucingamira podza pako; kukuutsira iwe mizimu, ngakhale onse akuru akuru a dziko lapansi; kukweza kucokera m'mipando yao mafumu onse a amitundu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 14

Onani Yesaya 14:9 nkhani