Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 13:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani tsiku la Yehova lidza, lankhanza, ndi mkwiyo ndi kukalipira kwaukali; kupasula dziko, ndi kudzaonongamo akucimwa psiti.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 13

Onani Yesaya 13:9 nkhani