Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 13:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Katundu wa Babulo, imene anaiona Yesaya mwana wa Amozi.

2. Kwezani mbendera pa phiri loti se, kwezani mau kwa iwo, kodolani kuti alowe m'zipata za akuru.

3. Ine ndalamulira opatulidwa anga, inde, ndaitana amphamvu anga, acite mkwiyo wanga, okondwerera ndi ukuru wanga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 13