Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 10:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Ambuye; Yehova wa makamu, Inu anthu anga okhala m'Ziyoni, musaope Asuri; ngakhale amenya inu ndi cibonga, kapena kukusamulira iwe ndodo yace, monga amacitira Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10

Onani Yesaya 10:24 nkhani