Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 10:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Tsoka kwa iwo amene alamulira malamulo osalungama, ndi kwa alembi olemba mphulupulu;

2. kuwapatulira osowa kuciweruziro, ndi kucotsera anthu anga aumphawi zoyenera zao, kuti alande za akazi amasiye, nafunkhire ana amasiye!

Werengani mutu wathunthu Yesaya 10