Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwana wamkazi wa Ziyoni wasiyidwa ngati citando ca m'munda wamphesa, ngati cilindo ca m'munda wamankhaka, ngati mudzi wozingidwa ndi nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:8 nkhani