Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 1:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akuru ako apanduka, ali anzao a mbala; onse akonda mitulo, natsata zokometsera mirandu; iwo saweruzira amasiye; ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye suwafika.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:23 nkhani