Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 1:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tiyeni, tsono, tiweruzane, ati Yehova; ngakhale zoipa zanu ziri zofiira, zidzayera ngati matalala; ngakhale ziri zofiira ngati kapezi, zidzakhala ngati ubweya wa nkhosa, woti mbu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:18 nkhani