Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musadze nazonso, nsembe zacabecabe; nsembe zofukiza zindinyansa; tsiku lokhala mwezi ndi sabata, kumema masonkhano, sindingalole mphulupulu ndi masonkhano.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:13 nkhani