Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nditani nazo nsembe zanu zocurukazo? ati Yehova; ndakhuta nazo nsembe zopsereza za nkhosa zamphongo ndi mafuta a nyama zonenepa; sindisekera ndi mwazi wa ng'ombe zamphongo, ngakhale wa ana a nkhosa, ngakhale wa atonde.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 1

Onani Yesaya 1:11 nkhani