Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 9:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aigupto, ndi Yuda, ndi Edomu, ndi ana a Amoni, ndi a Moabu, ndi onse ometa m'mphepete mwa tsitsi lao, okhala m'cipululu; pakuti amitundu onse ali osadulidwa, ndi nyumba ya Israyeli iri Yosadulidwa m'mtima.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 9

Onani Yeremiya 9:26 nkhani