Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 9:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mau a kulira amveka m'Ziyoni, Tafunkhidwa, tanyazitsidwa, pakuti tasiya dziko, pakuti agwetsa zokhalamo zathu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 9

Onani Yeremiya 9:19 nkhani