Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca mapiri ndidzagwa misozi ndi kulira, cifukwa ca mabusa a cipululu ndidzacita maliro, cifukwa apserera, kuti anthu sangathe kupitirirapo; ndiponso anthu sangathe kumva mau a ng'ombe zao; mbalame za mlengalenga ndi nyama zathawa, zapita.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 9

Onani Yeremiya 9:10 nkhani