Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinachera khutu, ndinamva koma sananena bwino; panalibe munthu amene anatembenuka kusiya zoipa zace, ndi kuti, Ndacita ciani? yense anatembenukira njira yace, monga akavalo athamangira m'nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 8

Onani Yeremiya 8:6 nkhani