Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 7:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo udzati kwa iwo, Umene ndi mtundu wosamvera mau a Yehova Mulungu wao, wosalola kulangizidwa, coonadi catha, cadulidwa pakamwa pao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 7

Onani Yeremiya 7:28 nkhani