Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pitani tsopano ku malo anga amene anali m'Silo, m'mene ndinaikamo dzina langa poyamba paja, ndi kuona cimene ndinacitira cifukwa ca zoipa za anthu anga Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 7

Onani Yeremiya 7:12 nkhani