Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 52:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Nebuzaradani kapitao wa alonda anatenga ndende anthu aumphawi, ndi anthu otsala amene anatsala m'mudzi, ndi amene anapandukira, kutsata mfumu ya ku Babulo, ndi otsala a unyinjiwo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 52

Onani Yeremiya 52:15 nkhani