Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 52:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwezi wacisanu, tsiku lakhumi la mwezi, ndico caka cakhumi ndi cisanu ndi cinai ca Nebukadirezara, mfumu ya ku Babulo, analowa m'Yerusalemu Nebuzaradani kapitao wa alonda, amene anaimirira pamaso pa mfumu ya ku Babulo:

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 52

Onani Yeremiya 52:12 nkhani