Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 51:58 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wa makamu atero: Makoma otakata a Babulo adzagwetsedwa ndithu, ndi zitseko zace zazitari zidzatenthedwa ndi moto; anthu adzagwirira nchito cabe, ndi mitundu ya anthu idzagwirira moto, nidzatopa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:58 nkhani