Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 51:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, ndimenyana ndi iwe, iwe phiri lakuononga, ati Yehova, limene liononga dziko lonse; ndipo ndidzakutambasulira iwe dzanja langa, ndipo ndidzakugubuduza iwe kumatanthwe, ndipo ndidzakuyesa iwe phiri lotenthedwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:25 nkhani