Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 51:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzatuma ku Babulo alendo, amene adzamkupira iye, amene adzataya zonse m'dziko lace, pakuti tsiku la cisauko adzamenyana ndi iye pomzungulira pace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:2 nkhani