Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 51:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu onse ali opulukira ndi opanda nzeru; wakusula golidi acitidwa manyazi ndi fanizo lace losema; pakuti fanizo lace loyenga liri bodza, mulibe mpweya m'menemo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:17 nkhani