Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 50:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onse amene anazipeza anazidya; adani ao anati, Sitiparamula mlandu, cifukwa iwo anacimwira Yehova, ndiye mokhalamo zolungama, Yehova, ciyembekezo ca atate ao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:7 nkhani