Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 50:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, mtundu uja adzakwerera mudzi wolimba ngati mkango wocokera ku Yordano wosefuka; koma dzidzidzi ndidzauthamangitsa umcokere, ndipo ali yense amene asankhidwa, ndidzamuika woyang'anira wace; pakuti wakunga Ine ndani? adzandiikira nthawi ndani? ndipo mbusa adzaima pamaso panga ndani?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:44 nkhani