Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 50:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Agwira uta ndi nthungo; ali ankharwe, alibe cifundo; mau ao apokosera ngati nyanja, ndipo akwera akavalo, yense aguba monga munthu wa kunkhondo, kukamenyana ndi iwe, mwana wamkazi wa Babulo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:42 nkhani