Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 50:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku omwewo, nthawi yomweyo, ati Yehova, zoipa za Israyeli zidzafunidwa, koma zidzasoweka; ndi zocimwa za Yuda, koma sizidzapezeka; pakuti ndidzakhululukira iwo amene ndidzawasiya ngati cotsala.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:20 nkhani