Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 5:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anenepa, anyezimira; inde apitiriza kucita zoipa; sanenera ana amasiye mlandu wao, kuti apindule; mlandu wa aumphawi saweruza.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:28 nkhani