Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Thawani inu, bwerani, khalani mwakuya, inu okhala m'Dedani; pakuti ndidzatengera pa iye tsoka la Esau, nthawi yoti ndidzamlanga iye.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:8 nkhani