Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, adzafika nadzauluka ngati ciombankhanga, adzatambasulira Boma mapiko ace, ndipo tsiku lomwelo mtima wa anthu amphamvu a Edomu adzakhala ngati mtima wa mkazi alinkudwala.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:22 nkhani