Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma za kuopsya kwako, kunyada kwa mtima wako kunakunyenga iwe, wokhala m'mapanga a thanthwe, woumirira msanje wa citunda, ngakhale usanja cisanja cako pamwamba penipeni ngati ciombankhanga, ndidzakutsitsa iwe kumeneko, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:16 nkhani