Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 48:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wakufunkha adzafikira pa midzi yonse, sudzapulumuka mudzi uli wonse; cigwa comwe cidzasakazidwa, ndipo cidikha cidzaonongedwa; monga wanena Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48

Onani Yeremiya 48:8 nkhani